Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 18:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Muubwezere, monganso uwu unabwezera, ndipo muwirikize kawiri, monga mwa nchito zace; m'cikhomo unathiramo, muuthirire cowirikiza.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 18

Onani Cibvumbulutso 18:6 nkhani