Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 18:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mngelo wolimba ananyamula mwala, ngati mphero yaikuru, naiponya m'nyanja, nanena, Cotero Babulo, mudzi waukuru, udzapasulidwa kolimba, ndipo sudzapezedwanso konse.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 18

Onani Cibvumbulutso 18:21 nkhani