Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 18:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndi kinamomo ndi amomo, ndi zofukiza, ndi zodzola, ndi libano, ndi vinyo, ndi mafuta, ndi ufa wosalala, ndi tirigu, ndi ng'ombe, ndi nkhosa; ndi malonda a akavalo, ndi a magareta, ndi a anthu ndi a miyoyo ya anthu.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 18

Onani Cibvumbulutso 18:13 nkhani