Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 18:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

malonda a golidi, ndi a siliva, ndi a mwala wa mtengo wace, ndi a ngale, ndi a nsaru yabafuta, ndi a cibakuwa, ndi a yonyezimira, ndi a mlangali; ndi mitengo yonse ya pfungo lokoma, ndi cotengera ciri conse ca minyanga ya njobvu, ndi cotengera ciri conse camtengo wa mtengo wace wapatali, ndi camkuwa ndi cacitsulo, ndi cansangalabwi;

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 18

Onani Cibvumbulutso 18:12 nkhani