Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 17:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cirombo cimene unaciona cinaliko, koma kulibe; ndipo cidzaturuka m'phompho, ndi kunka kucitayiko. Ndipo adzazizwa iwo akukhala padziko amene dzina lao silinalembedwa m'buku la moyo ciyambire makhazikidwe a dziko lapansi, pakuona cirombo, kuti cinaliko, ndipo kulibe, ndipo cidzakhalako.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 17

Onani Cibvumbulutso 17:8 nkhani