Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 17:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mngelo anati kwa ine, Uzizwa cifukwa ninji? ine ndidzakuuza iwe cinsinsi ca mkazi, ndi ca cirombo cakumbereka iye, cokhala nayo mitu isanu ndi iwiri ndi nyanga khumi.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 17

Onani Cibvumbulutso 17:7 nkhani