Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 16:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo waciwiri anatsanulira mbale yace m'nyanja; ndipo kunakhala mwazi ngati wa munthu wakufa; ndipo zamoyo zonse za m'nyanja zidafa.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 16

Onani Cibvumbulutso 16:3 nkhani