Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 16:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anacoka woyamba, natsanulira mbale yace kudziko; ndipo kunakhala cironda coipa ndi cosautsa pa anthu akukhala nalo lemba la cirombo nalambira fano lace.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 16

Onani Cibvumbulutso 16:2 nkhani