Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 16:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndinaona moturuka m'kamwa mwa cinjoka, ndi m'kamwa mwa cirombo, ndi m'kamwa mwa mneneri wonyenga mizimu itatu yonyansa, ngati acule;

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 16

Onani Cibvumbulutso 16:13 nkhani