Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 16:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo wacisanu ndi cimodzi anatsanulira mbale yace pa mtsinje waukuru Firate; ndi madzi ace anaphwa, kuti ikonzeke njira ya mafumu ocokera poturuka dzuwa.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 16

Onani Cibvumbulutso 16:12 nkhani