Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 15:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anaturuka m'Kacisi angelo asanu ndi awiri akukhala nayo miliri isanu ndi iwiri, atabvala mwala woyera, ndi wonyezimira, namangira malamba agolidi pacifuwa pao,

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 15

Onani Cibvumbulutso 15:6 nkhani