Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 15:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ayimba nyimbo ya Mose kapolo wa Mulungu, ndi nyimbo ya Mwanawankhosa, nanena, Nchito zanu nzazikuru ndi zozizwitsa, Ambuye Mulungu, Wamphamvuyonse; njira zanu nzolungama ndi zoona, Mfumu Inu ya nthawi zosatha.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 15

Onani Cibvumbulutso 15:3 nkhani