Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 14:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mngelo wina anaturuka pa guwa la nsembe, ndiye wakukhala nao ulamuliro pamoto; napfuula ndi mau akuru kwa iye wakukhala nalo zenga lakuthwa, nanena, 1 Tumiza zenga lako lakuthwa, nudule matsango a munda wampesa wa m'dziko; pakuti mphesa zace zapsa ndithu.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 14

Onani Cibvumbulutso 14:18 nkhani