Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 14:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndinamva mau ocokera Kumwamba, ndi kunena, Lemba, Odala akufa akumwalira mwa Ambuye, kuyambira tsopano; inde, anena Mzimu, kuti akapumule ku zolemetsa zao; pakuti nchito zao zitsatana nao pamodzi.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 14

Onani Cibvumbulutso 14:13 nkhani