Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 13:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anacipatsa ico kucita nkhondo ndi oyera mtima, ndi kuwalaka; ndipo anacipatsa ulamuliro wa pa pfuko liri lonse, ndi anthu, ndi manenedwe, ndi mitundu.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 13

Onani Cibvumbulutso 13:7 nkhani