Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 13:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo umodzi wa mitu yace unakhala ngati unalasidwa kufikira imfa; ndipo bala lace la kuimfa lidapola; ndipo dziko lonse linazizwa potsata ciromboco;

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 13

Onani Cibvumbulutso 13:3 nkhani