Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 13:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo cirombo ndinacionaco cinafanana ndi nyalugwe, ndi mapazi ace ngati mapazi a fisi, ndi pakamwa pace ngati pakamwa pa mkango; ndipo cinjoka cinampatsa iye mphamvu yace, ndi mpando wacifumu wace, ndi ulamuliro waukuru.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 13

Onani Cibvumbulutso 13:2 nkhani