Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 12:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo cinaponyedwa pansi cinjoka cacikuru, njoka yokalambayo, iye wochedwa mdierekezi ndi Satana, wonyenga wa dziko lonse; cinaponyedwa pansi kudziko, ndi angelo ace anaponyedwa naye pamodzi.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 12

Onani Cibvumbulutso 12:9 nkhani