Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 12:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo dziko linathandiza mkaziyo, ndi dziko linatsegula m'kamwa mwace, nilinameza madzi a mtsinje amene cinjoka cinalabvula m'kamwamwace.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 12

Onani Cibvumbulutso 12:16 nkhani