Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 12:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anapatsa mkazi mapiko awiri a ciombankhanga cacikuru, kuti akaulukire kucipululu, ku mbuto yace, kumene adyetsedwako nthawi, ndi zinthawi, ndi nusu la nthawi, osapenya nkhope ya njoka.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 12

Onani Cibvumbulutso 12:14 nkhani