Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 11:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anatsegulidwa Kacisi wa Mulungu amene ali m'Mwamba; ndipo linaoneka likasa la cipangano cace, m'Kacisi mwace, ndipo panali mphezi, ndi mau, ndi mabingu, ndi cibvomezi, ndi matalala akuru.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 11

Onani Cibvumbulutso 11:19 nkhani