Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Cibvumbulutso 1:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

3 cinsinsi ca nyenyezi zisanu ndi ziwiri zimene unaziona pa dzanja langa lamanja, ndi 4 zoikapo nyali zisanu ndi ziwiri zagolidi: nyenyezi zisanu ndi ziwiri ndizo 5 angelo a Mipingo isanu ndi iwirl; ndipo zoikapo nyali zisanu ndi ziwiri ndizo 6 Mipingo isanu ndi iwiri.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 1

Onani Cibvumbulutso 1:20 nkhani