Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Aroma 7:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo cifukwa cace, ngati iye akwatiwa ndi mwamuna wina, pokhala mwamuna wace wamoyo, adzanenedwa mkazi wacigololo; koma mwamunayo akafa, iye amasulidwa ku lamuloli; cotero sakhala wacigololo ngati akwatiwa ndi mwamuna wina.

Werengani mutu wathunthu Aroma 7

Onani Aroma 7:3 nkhani