Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Aroma 4:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace cilungamo cicokera m'cikhulupiriro, kuti cikhale monga mwa cisomo; kuti lonjezo likhale Iokhazikika kwa mbeu zonse; si kwa iwo a cilamulo okha okha, komakwa iwonso a cikhulupiriro ca Abrahamu; ndiye kholo la ife tonse;

Werengani mutu wathunthu Aroma 4

Onani Aroma 4:16 nkhani