Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Aroma 4:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndiponso kholo la mdulidwe wa iwo amene siali a mdulidwe okha, koma wa iwo amene atsata mayendedwe a cikhulupiriro cija ca kholo lathu Abrahamu, cimene iye anali naco asanadulidwe.

Werengani mutu wathunthu Aroma 4

Onani Aroma 4:12 nkhani