Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Aroma 4:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo iye analandira cizindikilo ca mdulidwe, ndico cosindikiza cilungamo ca cikhulupiriro, comwe iye anali naco asanadulidwe; kuti kotero iye akhale kholo la onse akukhulupira, angakhale iwo sanadulidwa, kuti cilungamo ciwerengedwe kwa iwonso;

Werengani mutu wathunthu Aroma 4

Onani Aroma 4:11 nkhani