Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Aroma 3:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ciani tsono? kodi tiposa ife? Iai ndithu; pakuti tidawaneneza kale Ayuda ndi Ahelene omwe, kuti onsewa agwidwa ndi ucimo;

Werengani mutu wathunthu Aroma 3

Onani Aroma 3:9 nkhani