Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Aroma 3:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo tilekerenji kunena, Ticite zoipa kuti zabwino zikadze (monganso ena atinamiza ndi kuti timanena)? Kulanga kwa amenewo kuli kolungama.

Werengani mutu wathunthu Aroma 3

Onani Aroma 3:8 nkhani