Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Aroma 16:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipereka kwa inu Febe, mlongo wathu, ndiye mtumiki wamkazi wa Mpingo wa Ambuye wa ku Kenkreya;

2. kuti mumlandire iye mwa Ambuye, monga kuyenera oyera mtima, ndi kuti mumthandize m'zinthu zili zonse adzazifuna kwa inu; pakuti iye yekha anali wosungira ambiri, ndi ine ndemwe.

Werengani mutu wathunthu Aroma 16