Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Aroma 16:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

kuti mumlandire iye mwa Ambuye, monga kuyenera oyera mtima, ndi kuti mumthandize m'zinthu zili zonse adzazifuna kwa inu; pakuti iye yekha anali wosungira ambiri, ndi ine ndemwe.

Werengani mutu wathunthu Aroma 16

Onani Aroma 16:2 nkhani