Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Aroma 14:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cikhulupiriro cimene uli naco, ukhale naco kwa iwe wekha pamaso pa Mulungu. Wodala ndiye amene sadziweruza mwini yekha m'zinthu zomwe iye wazibvomereza.

Werengani mutu wathunthu Aroma 14

Onani Aroma 14:22 nkhani