Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Aroma 1:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo cimodzimodzinso amuna anasiya macitidwe a cibadwidwe ca akazi, natenthetsana ndi colakalaka cao wina ndi mnzace, amuna okhaokha anacitirana camanyazi, ndipo analandira mwa iwo okha mphotho yakuyenera kulakwa kwao.

Werengani mutu wathunthu Aroma 1

Onani Aroma 1:27 nkhani