Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ahebri 8:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti ili ndi pangano ndidzalipangana ndi nyumba ya Israyeli,Atapita masiku ajawa, anena Ambuye:Ndidzapatsa malamulo anga kuwalonga m'nzeru zao,Ndipo pamtima pao ndidzawalemba iwo;Ndipo ndidzawakhalira iwo Mulungu,Ndipo iwo adzandikhalira Ine anthu:

Werengani mutu wathunthu Ahebri 8

Onani Ahebri 8:10 nkhani