Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ahebri 6:19-20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

19. cimene tiri naco ngati nangula wa moyo, cokhazikika ndi colimbanso, ndi cakulowa m'katikati mwa cophimba;

20. m'mene Yesu mtsogoleri analowamo cifukwa ca ife, atakhala mkulu wa ansembe nthawi yosatha monga mwa dongosolo la Melikizedeke.

Werengani mutu wathunthu Ahebri 6