Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ahebri 6:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

kuti mwa zinthu ziwiri zosasinthika, m'mene Mulungu sakhoza kunama, tikakhale naco coticenjeza colimba, ife amene tidathawira kucigwira ciyembekezo coikika pamaso pathu;

Werengani mutu wathunthu Ahebri 6

Onani Ahebri 6:18 nkhani