Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ahebri 6:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mwa ici, polekana nao mau a ciyambidwe ca Kristu, tipitirire kutsata ukulu msinkhu; osaikanso maziko a kutembenuka mtima kusiyana nazo nchito zakufa, ndi a cikhulupiriro ca pa Mulungu,

Werengani mutu wathunthu Ahebri 6

Onani Ahebri 6:1 nkhani