Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ahebri 2:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

tidzapulumuka bwanji ife, tikapanda kusamala cipulumutso cacikuru cotero? cimene Ambuye adayamba kucilankhula, ndipo iwo adacimva anatilimbikitsira ife;

Werengani mutu wathunthu Ahebri 2

Onani Ahebri 2:3 nkhani