Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ahebri 11:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi cikhulupiriro Nowa, pocenjezedwa ndi Mulungu za zinthu zisanapenyeke, ndi pocita mantha, anamanga cingalawa ca kupulumutsiramo iwo a m'nyumba yace; kumene anatsutsa nako dziko lapansi, nakhala wolowa nyumba wa cilungamo ciri monga mwa cikhulupiriro.

Werengani mutu wathunthu Ahebri 11

Onani Ahebri 11:7 nkhani