Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ahebri 10:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. mthunzi wa zokoma zirinkudza, osati cifaniziro ceni ceni ca zinthuzo, sicikhozatu, ndi nsembe zomwezi caka ndi caka, zimene azipereka kosalekeza, kuwayesera angwiro iwo akuyandikira.

2. Pakadapanda kutero, kodi sakadaleka kuzipereka, cifukwa otumikirawo sakadakhala naco cikumbu mtima ca macimo, popeza adayeretsedwa kamodzi?

3. Komatu mu izizo muli cikumbukiro ca macimo caka ndi caka.

Werengani mutu wathunthu Ahebri 10