Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ahebri 1:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ameneyo, pokhala ali cinyezimiro ca ulemerero wace, ndi cizindikilo ceni ceni ca cikhalidwe cace, nanyamula zonse ndi mau a mphamvu yace, m'mene adacita ciyeretso ca zoipa, anakhala pa dzanja lamanja la Ukulu m'Mwamba,

Werengani mutu wathunthu Ahebri 1

Onani Ahebri 1:3 nkhani