Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Agalatiya 5:18-20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

18. Ngati Mzimu akutsogolerani, simuli omvera lamulo.

19. Ndipo nchito za thupi zionekera, ndizo dama, codetsa, kukhumba zonyansa, kupembedza mafano,

20. nyanga, madano, ndeu, kaduka, zopsa mtima, zotetana, magawano, mipatuko, njiru,

Werengani mutu wathunthu Agalatiya 5