Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Agalatiya 5:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti thupi lilakalaka potsutsana naye Mzimu, ndi Mzimu potsutsana nalo thupi; pakuti izi sizilingana; kuti zimene muzifuna musazicite.

Werengani mutu wathunthu Agalatiya 5

Onani Agalatiya 5:17 nkhani