Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Agalatiya 2:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma ngati ife, pofuna kuyesedwa olungama mwa Kristu, tipezedwanso tiri ocimwa tokha, kodi Kristu ali mtumikiwa ucimo cifukwa cace? Msatero ai.

Werengani mutu wathunthu Agalatiya 2

Onani Agalatiya 2:17 nkhani