Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Agalatiya 2:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

koma podziwa kuti munthu sayesedwa wolungama pa: nchito ya lamulo, koma mwa cikhulupiriro ca Yesu Kristu, ifedi tinakhulupirira kwa Yesu Kristu, kuti tikayesedwe olungama ndicikhulupiriro ca Kristu, ndipo si ndi nchito za lamulo; pakuti palibe munthu adzayesedwa wolungama ndi nchito za lamulo.

Werengani mutu wathunthu Agalatiya 2

Onani Agalatiya 2:16 nkhani