Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Afilipi 4:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Potero, abale anga okondedwa, olakalakidwa, ndinu cimwemwe canga ndikorona wanga, cirimikani motere mwa Ambuye, okondedwa.

Werengani mutu wathunthu Afilipi 4

Onani Afilipi 4:1 nkhani