Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Afilipi 3:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

amene adzasanduliza thupi lathu lopepulidwa, lifanane nalo thupi lace la ulemerero, monga mwa macitidwe amene akhoza kudzigonjetsera nao zinthu zonse.

Werengani mutu wathunthu Afilipi 3

Onani Afilipi 3:21 nkhani