Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Aefeso 2:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

kuti nthawi ija munali opanda Kristu, alendo a padera ndi mbumba ya Israyeli, ndi alendo alibe kanthu ndi mapangano a malonjezano, opanda ciyembekezo, ndi opanda Mulungu m'dziko lapansi.

Werengani mutu wathunthu Aefeso 2

Onani Aefeso 2:12 nkhani