Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

3 Yohane 1:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Momwemo, ndikadza ine, ndidzakumbutsa nchito zace zimene aeitazi, zakunena zopanda pace pa ife ndi mau oipa; ndipopopeza izi sizimkwanira, salandira abale iye yekha, ndipo ofuna kuwalandira awaletsa, nawataya kunja powaturutsa mu Mpingo,

Werengani mutu wathunthu 3 Yohane 1

Onani 3 Yohane 1:10 nkhani