Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Yohane 1:11-13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

11. Pakuti iye wakumlankhula ayanjana nazo nchito zace zoipa.

12. Pokhala ndiri nazo zambiri zakukulemberani, sindifuna kucita ndi kalata ndi kapezi; koma ndiyembekeza kudza kwa inu, ndi kulankhula popenyana, kuti cimwemwecanucikwanire.

13. Akulankhulani ana a mbale wanu wosankhika.

Werengani mutu wathunthu 2 Yohane 1