Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Yohane 1:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pokhala ndiri nazo zambiri zakukulemberani, sindifuna kucita ndi kalata ndi kapezi; koma ndiyembekeza kudza kwa inu, ndi kulankhula popenyana, kuti cimwemwecanucikwanire.

Werengani mutu wathunthu 2 Yohane 1

Onani 2 Yohane 1:12 nkhani